Masalmo 142:6-7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

6. Tamverani kupfuula kwanga; papeza ndisauka kwambiri;Ndilanditseni kwa iwo akundilondola; popeza andilaka.

7. Turutsani moyo wanga m'ndende, kuti ndiyamike dzina lanu;Olungama adzandizinga;Pakuti mudzandicitira zokoma.

Masalmo 142