Masalmo 141:9-10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Mundisunge ndisagwe mumsampha anandicherawo,Ndisakodwe m'makwekwe a iwo ocita zopanda pace,

10. Oipa agwe pamodzi m'maukonde ao,Kufikira nditapitirira ine.

Masalmo 141