Masalmo 139:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Munandisanthula, Yehova, nimundidziwa.

2. Inumudziwakukhalakwangandi kuuka kwanga,Muzindikira lingaliro langa muli kutali.

3. Muyesa popita ine ndi pogona ine,Ndi njira zanga zonse muzolowerana nazo.

Masalmo 139