Masalmo 137:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ku mitsinje ya ku Babulo,Kumeneko tinakhala pansi, inde tinalira,Pokumbukila Ziyoni.

2. Pa msondodzi uli m'mwemo Tinapacika mazeze athu.

Masalmo 137