Masalmo 136:24-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. Natikwatula kwa otisautsa;Pakuti cifundo cace ncosatha.

25. Ndiye wakupatsa nyama zonse cakudya;Pakuti cifundo cace ncosatha.

26. Yamikani Mulungu wa kumwamba,Pakuti cifundo cace ncosatha.

Masalmo 136