Masalmo 128:4-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

4. Taonani, m'mwemo adzadalitsikaMunthu wakuopa Yehova.

5. Yehova adzakudalitsa ali m'ZiyoniNdipo udzaona zokoma za Yerusalemu masiku onse a moyo wako.

6. Inde, udzaona zidzukulu zako.Mtendere ukhale ndi Israyeli.

Masalmo 128