Masalmo 128:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Wodala yense wakuopa Yehova, Wakuyenda m'njira zace.

2. Pakuti udzadya za nchito ya manja ako;Wodala iwe, ndipo kudzakukomera.

Masalmo 128