Masalmo 124:5-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

5. Madzi odzikuza akadapita pa moyo wathu.

6. Alemekezedwe Yehova,Amene sanatipereka kumano kwao tikhale cakudya cao.

7. Moyo wathu unaonjoka ngati mbalame mu msampha wa msodzi;Msampha unatyoka ndi ife tinaonioka.

8. Thandizo lathu liri m'dzina la Yehova,Wolenga kumwamba ndi dziko lapansi.

Masalmo 124