Masalmo 124:1-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Akadapanda kukhala nafe Yehova,Anene tsono Israyeli; Akadapanda kukhala nafe Yehova,Pakutiukira anthu: