Masalmo 123:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndikweza maso anga kwa Inu,Kwa Inu wakukhala kumwamba.

2. Taonani, monga maso a anyamata ayang'anira dzanja la ambuye ao,Monga maso a adzakazi ayang'anira dzanja la mbuye wao wamkazi:Momwemo maso athu ayang'anira Yehova Mulungu wathu,Kufikira aticitira cifundo.

Masalmo 123