Masalmo 119:58-60 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

58. Ndinapemba pankhope panu ndi mtima wanga wonse:Mundicitire cifundo monga mwa mau anu.

59. Ndinaganizira njira zanga,Ndipo ndinabweza mapazi anga atsate mboni zanu.

60. Ndinafulumira, osacedwa,Kusamalira malamulo anu.

Masalmo 119