Masalmo 119:36-38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

36. Lingitsani mtima wanga ku mboni zanu,Si ku cisiriro ai.

37. Mucititse mlubza maso anga ndisapenye zacabe,Mundipatse moyo mu njira yanu.

38. Limbitsirani mtumiki wanu mau anu,Ndiye wodzipereka kukuopani.

Masalmo 119