Masalmo 119:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Odala angwiro m'mayendedwe ao,Akuyenda m'cilamulo ca Yehova.

2. Odala iwo akusunga mboni zace,Akumfuna ndi mtima wonse;

3. Inde, sacita cosalungama;Ayenda m'njira zace.

4. Inu munatilamulira.Tisamalire malangizo anu ndi cangu,

Masalmo 119