Masalmo 118:28-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

28. Inu ndinu Mulungu wanga, ndipo ndidzakuyamikani;Ndinu Mulungu wanga, ndidzakukwezani.

29. Yamikani Yehova, pakuti Iye ndiye wabwino,Pakuti cifundo cace ncosatha.

Masalmo 118