Masalmo 118:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Yamikani Yehova; pakuti Iye ndiye wabwino;Pakuti cifundo cace ncosatha.

2. Anene tsono Israyeli,Kuti cifundo cace ncosatha.

3. Anene tsono nyumba ya Aroni,Kuti cifundo cace ncosatha.

4. Anene tsono iwo akuopa Yehova,Kuti cifundo cace ncosatha.

Masalmo 118