Masalmo 118:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Yamikani Yehova; pakuti Iye ndiye wabwino;Pakuti cifundo cace ncosatha.

2. Anene tsono Israyeli,Kuti cifundo cace ncosatha.

Masalmo 118