Masalmo 115:17-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Akufa salemekeza Yehova,Kapena ali yense wakutsikira kuli cete: Koma ife tidzalemekeza YehovaKuyambira tsopano