Masalmo 11:6-7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

6. Adzagwetsa pwata pwata misampha pa oipa;Moto ndi miyala yasuifure, ndi mphepo yoopsa zidzawagawikira m'cikho cao.

7. Pakuti Yehova ndiye wolungama; akonda zolungama:Woongoka mtima adzapenya nkhope yace.

Masalmo 11