Masalmo 106:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Haleluya.Yamikani Yehova; pakuti Iye ndiye wabwino:Pakuti cifundo cace ncosatha.

2. Adzafotokoza ndani nchito zamphamvu za Yehova,Adzamveketsa ndani cilemekezo cace conse?

3. Odala iwo amene asunga ciweruzo,Iye amene acita cilungamo nthawi zonse.

Masalmo 106