Masalmo 102:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musandibisire nkhope yanu tsiku la nsautso yanga;Mundichereze khutu lanu;Tsiku limene ndiitana ine mundiyankhe msanga,

Masalmo 102

Masalmo 102:1-11