Masalmo 100:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Pfuulirani kwa Yehova, inu, dziko lonse lapansi. Tumikirani Yehova ndi cikondwerero:Idzani pamaso pace ndi