Masalmo 1:4-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

4. Oipa satero ai;Koma akunga mungu wouluka ndi mphepo.

5. Cifukwa cace oipa sadzaimirira pa mlanduwo,Kapena ocimwa mu msonkhano wa olungama.

6. Pakuti Yehova adziwa mayendedwe a olungama;Koma mayendedwe a oipa adzatayika.

Masalmo 1