Marko 7:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadabwa kwakukurukuru, nanena, Wacita Iye zonse bwino; angakhale ogontha awamvetsa, ndi osalankhula awalankhulitsa.

Marko 7

Marko 7:35-37