Marko 7:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaturukanso m'maiko a ku Turo, nadzera pakati pa Sidoni, cufikira ku nyanja ya Galileya, ndi cupyola pakati pa maiko a ku Dekapolio

Marko 7

Marko 7:25-35