Marko 5:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo anafika tsidya lina la nyanja, ku dziko la Agerasa,

2. Ndipo pameneadaturuka mungalawa, pomwepo anakomana naye munthu woturuka kumanda wa mzimu wonyansa,

Marko 5