Marko 16:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaturuka iwo, nathawa kumanda; pakuti kunthunthumira ndi kudabwa kwakukuru kudawagwira; ndipo sanauza kanthu kwa munthu ali yense; pakuti anacitamantha.

Marko 16

Marko 16:1-13