Marko 13:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace dikirani; pakuti simudziwa inu nthawi yace yakubwera mwini nyumba, kapena madzulo, kapena pakati pausiku, kapena pakulira tambala, kapena mamawa;

Marko 13

Marko 13:32-36