Marko 13:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo phunzirani ndi mkuyu fanizo lace; pamene pafika kuti nthambi yace ikhala yanthete, ndipo anaphuka masamba ace, muzindikira kuti layandikira dzinja;

Marko 13

Marko 13:21-32