Marko 12:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yesu anati kwa iwo, Perekani zace za Kaisara kwa Kaisara, ndi zace za Mulungu kwa Mulungu. Ndipo anazizwa naye kwambiri.

Marko 12

Marko 12:15-24