Maliro 3:63-66 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

63. Taonani kukhala ndi kunyamuka kwao; ndine nyimbo yao.

64. Mudzawabwezera cilango, Yehova, monga mwa macitidwe a manja ao;

65. Muphimbe mtima wao ndi kuwatemberera;

66. Mudzawalondola mokwiya ndi kuwaononga pansi pa thambo la Yehova.

Maliro 3