Maliro 3:36-38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

36. Kukhotetsa mlandu wa munthu, zonsezi Ambuye sazikonda.

37. Ndani anganene, conena cace ndi kucitikadi, ngati Ambuye salamulira?

38. Kodi m'kamwa mwa Wam'mwambamwamba simuturuka zobvuta ndi zabwino?

Maliro 3