Macitidwe 5:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma munthu wina dzina lace Hananiya pamodzi ndi Safira mkazi wace,

2. anagulitsa cao, napatula pa mtengo wace, mkazi yemwe anadziwa, natenga cotsala, naciika pa mapazi a atumwi.

Macitidwe 5