Macitidwe 3:19-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. Cifukwa cace lapani, bwererani kuti afafanizidwe macimo anu, kotero kuti zidze nyengo zakutsitsimutsa zocokera ku nkhope ya Ambuye;

20. ndipo atume amene anaikidwa kwa inu, Kristu Yesu;

21. amene thambo la kumwamba liyenera kumlandira kufikira nthawi zakukonzanso zinthu zonse, zimene Mulunguanalankhula za izo m'kamwa mwa aneneri ace oyera ciyambire.

Macitidwe 3