Macitidwe 26:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

komatu kuyambira kwa iwo a m'Damasiko, ndi a m'Yerusalemu, ndi m'dziko lonse la Yudeya, ndi kwa amitundunso ndinalalikira kuti alape, natembenukire kwa Mulungu, ndi kucita nchito zoyenera kutembenuka mtima.

Macitidwe 26

Macitidwe 26:12-24