Macitidwe 25:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'mawa mwace tsono, atafika Agripa ndi Bemike ndi cifumu cacikuru, ndipo atalowa momvera milandu, pamodzi ndi akapitao akuru, ndi amuna omveka a mudziwo, ndipo pakulamulira Festo, anadza naye Paulo.

Macitidwe 25

Macitidwe 25:14-26