Macitidwe 1:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Komatu mudzalandira mphamvu, Mzimu Woyera atadza pa inu: ndipo mudzakhala mboni zanga m'Yerusalemu, ndi m'Yudeya lonse, ndi m'Samariya, ndi kufikira malekezero ace a dziko.

Macitidwe 1

Macitidwe 1:1-17