Luka 3:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Herode mfumu ija, m'mene Yohane anamdzudzula cifukwa ca Herodiya, mkazi wa mbale wace, ndi ca zinthu zonse zoina Herode anazicita,

Luka 3

Luka 3:15-28