Luka 3:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma iye anayankha nanena kwa iwo, Iye amene ali nao malaya awiri apatse kwa iye amene alibe; ndi iye amene ali nazo zakudya acite comweco.

Luka 3

Luka 3:6-17