Luka 22:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa iwo, Pamene ndinakutumizani opanda thumba la ndalama, ndi thumba la kamba, ndi nsapato, munasowa kanthu kodi? Anati iwo, Iai.

Luka 22

Luka 22:31-40