Luka 21:37-38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

37. Ndipo usana uli wonse iye analikuphunzitsa m'Kacisi; ndi usiku uli wonse anaturuka, nagona pa phiri lochedwa la Azitona.

38. Ndipo anthu onse analawira mamawa kudza kwa iye kuKacisi kudzamvera Iye.

Luka 21