Luka 21:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma zisanacitike izi, anthu adzakuthirani manja, nadzakuzunzani, nadzapereka inu ku masunagoge ndi ndende, nadzamuka nanu kwa mafumu ndi akazembe, cifukwa ca dzina langa.

Luka 21

Luka 21:2-22