Luka 20:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatsutsana mwa okha, nanena, Ngati tinena ucokera Kumwamba; adzati, Simunamkhulupirira cifukwa ninji?

Luka 20

Luka 20:1-8