Luka 19:17-19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. Ndipo anati kwa iye, Cabwino, kapolo wabwino iwe; popeza unakhala wokhulupirika m'cacing'onong'ono, khala nao ulamuliro pa midzi khumi.

18. Ndipo anadza waciwiri, nanena, Mbuye, ndalama yanu yapindula ndalama zisanu.

19. Ndipo anati kwa iyenso, Khala iwenso woweruza midzi isanu.

Luka 19