Luka 18:42-43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

42. Ndipo Yesu anati kwa iye, Penyanso: cikhulupiriro cako cakupulumutsa iwe.

43. Ndipo pomwepo anapenyanso, namtsata iye, ndi kulemekeza Mulungu: ndipo anthu onse pakuona, anacitira Mulungu mayamiko.

Luka 18