Luka 17:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo anati kwa ophunzira ace, Sikutheka kuti zolakwitsa zisadze; koma tsoka iye amene adza nazo.

2. Kukolowekedwa mwala wamphero m'khosi mwace ndi kuponyedwa Iye m'nyanja nkwapafupi, koma kulakwitsa mmodzi wa ang'ono awa nkwapatali.

3. Kadzicenjerani nokha; akacimwa mbale wako umdzudzule; akalapa, umkhululukire.

Luka 17