Luka 16:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kapitao uyu anati mumtima mwace, Ndidzacita ciani, cifukwa mbuye wanga andicotsera ukapitao? kulima ndiribe mphamvu, kupemphapempha kundicititsa manyazi.

Luka 16

Luka 16:1-10