Luka 11:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene pali ponse mzimu wonyansa ukaturuka mwa munthu, upyola malo opanda madzi nufunafuna mpumulo; ndipo posaupeza unena, Ndidzabwera kunyumba kwanga kumene ndinaturukako;

Luka 11

Luka 11:18-26