Levitiko 5:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kapena munthu akakhudza ciri conse codetsa kapena mtembo wa nyama yodetsa, kapena mtembo wa coweta codetsa, kapena mtembo wa cokwawa codetsa, kungakhale kudambisikira, ali wodetsedwa, ndi woparamula.

Levitiko 5

Levitiko 5:1-6