Levitiko 25:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Monga mwa kucuruka kwa zaka zace uonjeze mtengo wace, ndi monga mwa kucepa kwa zaka zace ucepse mtengo wace; pakuti akugulitsa powerenga masiku ace.

Levitiko 25

Levitiko 25:12-19