Levitiko 22:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo musamazilandira izi ku dzanja la mlendo ndi kubwera nazo zikhale cakudya ca Mulungu wanu; popeza ziri nako kubvunda kwao; ziri ndi cirema; sizidzalandirikira inu.

Levitiko 22

Levitiko 22:23-33